Anthu atatu afa ndipo m’modzi akulandira thandizo la ku chipatala galimoto la mtundu wa Mazda Axela Hatchback litawagunda Lolemba m’mawa m’boma la Mangochi. Ofalitsankhani wa...
“Achinyamata ambiri m’boma la Ntchisi ali ndi luso lozama pa masewero,” awa ndi mawu amene ayankhula a Anderson Msonthi amene akuthandiza masewero a mpira wamiyendo...
Anthu ochuluka akhamukira ku bwalo lamasewero la pa msika wa Area 24 ku Lilongwe komwe kukhale msonkhano wa chipani cha Malawi Congress (MCP). Pakadali pano,...
Mabanja okwana makumi asanu ammudzi mwa mfumu yaikulu Masumbakhunda ozungulira khalango ya Dzalanyama m’boma la Lilongwe ali ndi chimwemwe atalandira mbaula zamakono zoyendera mphamvu ya...
Bungwe la Small Holder Farmers Fertilizer Revolving Fund of Malawi (SFFRFM) lati zokonzekera zokhudza ntchito yogulitsa feteleza wotsika mtengo mundondomeko ya boma ya AIP zikuyenda...
Bungwe la Immigration lati pakufunika mgwirizano polimbikitsa aMalawi kuti azitsata malamulo pamene akupita maiko ena. M’modzi mwa adindo ku bungweli, a Fletcher Nyirenda, anayankhula izi...
Bungwe la Churches Action in Relief and Development (CARD) layamikira nyumba yowulutsa mawu ya Malawi Broadcasting Corporation (MBC) ponena kuti ndi akadaulo pantchito yawo. Mkulu...
Apolisi m’boma la Mangochi amanga anthu anayi amene akuwaganizira kuti anathyola ndi kuba zakumwa zaukali zandalama pafupifupi K2.3 million pa malo ena ogulitsira mowa otchedwa...
Dedza Police Traffic Section Head Inspector Finai Mwaighogha has challenged motorbike-taxi operators to adhere to road traffic rules to reduce road accidents in Dedza District....