Category : Nkhani
DR Usi apempha NEEF iganizire aphunzitsi
Wachiwiri kwa mtsogoleri wadziko lino, Dr Michael Usi, wapempha bungwe la NEEF kuti liganizire aphunzitsi aku pulaimale ndi ena akusekondale powatsekulira ngongole yawo yapadera yochitira...
Zokonzekera msonkhano wapachaka wa Surveyors Institute of Malawi zili mchimake
Bungwe la Surveyors Institute of Malawi lati chilichonse chili mchimake pa zokonzekera za msonkhano wawo waukulu wapachaka umene uyambe pa 26 mpakana pa 27 mwezi...
Madam Chakwera apempha mafumu kuti alimbikitse ana pa maphunziro
Mayi wa dziko lino, Madam Monica Chakwera, wapempha mafumu m’dziko muno kuti athandize kuwongola ana m’madera mwawo, powalimbikitsa sukulu m’malo mwa ukwati ndikuwazindikiritsa kuyipa kochita...
Boma layamikira ntchito za NASCENT Solutions polimbikitsa maphunziro
Unduna zamaphunziro wayamikira bungwe la Nascent Solutions kaamba kantchito yolimbikitsa maphunziro a nkomba phala msukulu komanso a sukulu ya kwacha m’dziko muno mu zaka zisanu...
Osagulitsa ndi kugula chiponde – Unduna wazaumoyo
Unduna wazaumoyo wachenjeza anthu kuti asiye mchitidwe ogulitsa ndi kugula chiponde kapena kuti “Ready to Use Therapeutic Food” mu chingerezi. Malinga ndi chikalata chomwe undunawu...
Oyendetsa galimoto wadzipereka atapha anyamata atatu
Anthu atatu afa ndipo m’modzi akulandira thandizo la ku chipatala galimoto la mtundu wa Mazda Axela Hatchback litawagunda Lolemba m’mawa m’boma la Mangochi. Ofalitsankhani wa...

