Bungwe la Chewa Heritage Malawi – Chifukwato cha a Chewa lauza a Enock Chihana kuti apepese mtundu wa a Chewa pazimene adayankhula pamsonkhano wa olembankhani...
Prezidenti wa dziko lino Dr Lazarus Chakwera watsimikizira anthu m’boma la Dowa kuti ntchito yopopa madzi m’nyanja ya Malawi ithandiza kubweretsa ukhondo ndi madzi pafupi...
Bwalo la milandu la First Grade Magistrate ku Karonga lagamula a Mussa Banda kuti akakhale kundende kwazaka zitatu ndikugwira ntchito yakalavula gaga chifukwa chopezeka olakwa...
Katundu yemwe bungwe la Malawi Council for Disability Affairs (MACODA) limayenera kugawa kwa anthu ovutika mdera la Mtanga kwa mfumu yaikulu Chimwala Ku Mangochi wakokoloka...
Ntchito yolemba mayina a anthu m’kaundula wa voti ili mkati pa sukulu ya pulayimare ya Manja ku Blantyre. Pamene MBC inayendera pa malowa inapeza kuti...