Category : Nkhani
‘Boma ligwirane manja ndi opanga fetereza wa Mbeya’
Kampani ya Nkhokwe Fertilizer Limited yapempha boma kuti liganizire zoyika feteleza wawo pa ndondomeko ya zipangizo zotsika mtengo za AIP chifukwa ali ndi kuthekera kobwezeretsa...
Kambwiri ayikidwa mmanda mawa
Thupi la amene anali mkhalakale pa nkhani zoulutsa mawu, Joshua Kambwiri, alitengera ku mudzi kwawo ku Domasi m’boma la Zomba, kumene akaliyike m’manda mawa Lolemba....
Osakhala, kuchita malonda pafupi ndi njanji — Boma
Boma lati anthu okhala komanso ochita malonda kufupi ndi njanji ali ndi udindo oteteza zipangizo za njanji kuti ntchito za sitima zipite patsogolo m’dziko muno....
Oimba aphunzire kugwira ntchito ndi aluso ena — Billy Kaunda
Billy Kaunda walangiza oimba kuti aphunzire kugwira ntchito ndi aluso ena monga alakatuli. Kaunda wayankhula izi pomwe wati akubwera ndi chimbale chatsopano posachedwapa momwe Okoma...

