Category : Nkhani
Boma lalimbikitsa ulimi
Unduna wa za ulimi wakhazikitsa ntchito yopereka feteleza wangongole kwa alimi a m’ma boma a Chikwawa ndi Nsanje. Ntchitoyi ili pansi pa bungwe la National...
‘Boma lithandiza onse’
Wachiwiri kwa mtsogoleri wa dziko lino, Dr Michael Usi, wati boma likuyesetsa kuti anthu onse amene akhudzidwa ndi njala akhale ndi chakudya posatengera dera limene...
MACRA ikuchita bwino — Suleman
Bungwe la Malawi Communications Regulatory Authority (MACRA) lamema anthu kuti aphunzire kuyamikira bungweli chifukwa likuyesetsa kutukula njira zamakono zofalitsira uthenga komanso kuteteza aMalawi ku uthenga...
MZUNI alumni yapereka K2.9M kwa ophunzira osowa
Ophunzira akale apa sukulu ya Mzuzu University apereka K2.9 million kwa ophunzira osowa apa sukuluyi ndicholinga chakuti iwathandizire fizi komanso zinthu zina. Amene wayimira mkulu...
Abambo awiri awapeza olakwa pamulandu wosakaza nkhalango
Bwalo la Senior Grade Magistrate ku Blantyre lachiwiri lapeza olakwa abambo awiri komanso kuwalanda belo chifukwa chopalamula milandu yozembetsa zinthu zamu nkhalango yotetezeka. Amuna awiriwa ...
Aphungu akhutira ndi ntchito ya NEEF
Aphungu anyumba ya malamulo m’chigawo chapakati ayamika ntchito yogawa fetereza wangongole amene bungwe la Economic Empowerment Fund (NEEF) likupereka kwa alimi. Mwa zina, aphunguwa amene...
AGCOM ikutukula alimi
Bungwe la Agriculture Commercialisation (AGCOM) lathandiza kutukula gulu la alimi limene akulitcha kuti ‘Team North Cooperative’ lochokera ku Lupaso munzinda wa Mzuzu. Poyankhula pamene nduna...

