Boma lalimbikitsa alimi m’dziko muno kugwiritsa bwino ntchito mwayi omwe awupeza wa feteleza wangongole kuchokera ku bungwe la National Economic Empowerment Fund (NEEF), ponena kuti...
Timu ya Ekhaya tsopano ili ndi mwayi waukulu olowa mu ligi yaikulu ya TNM kuchoka mu ligi ya mchigawo chakummwera pomwe tsopano ikungofuna ma poinsi...
Apolisi ku Mangochi amanga oyimba odziwika kuti Bandera koma dzina lake lenileni ndi Abdul-Karim Saidi pomuganizira kuti anasunga mokakamiza mtsikana wachichepere wazaka 14. Ofalitsankhani za...
Mtsogoleri wakale wa bungwe la Film Association of Malawi (FAMA), a Gift Sukali, wafunira zabwino atsogoleri atsopano amene bungweli lawasankha kumene. A Sukali ati ndi...
Bungwe la Malawi Network of Older Persons’ Organizations (MANEPO) lati ndi lokhudzidwa ndi kuchuluka kwa nkhanza zomwe achikulire akukumana nazo m’dziko muno kuphatikizapo kuwaganizira kuti...
Phungu wa kummwera kwa boma la Lilongwe, a Peter Dimba, wapempha mabungwe ndi aMalawi kuti agwirane manja ndi bungwe la National Economic Empowerment Fund (NEEF)...
Phungu wa kumpoto kwa boma la Mangochi, a Benedicto Chambo, wati ma boma a m’mbuyomu anamutaya ndipo sanalabadire ukadaulo wake pa ntchito za ulimi ndi...
Unduna waza umoyo wati walandira katemera wa matenda a cholera 720,185 wa mkamwa kuchokera ku bungwe laza umoyo pa dziko la World Health Organization (WHO)....
Mkulu wa ntchito za ndende m’chigawo cha pakati, a Bazirial Chapuwala, walamula ogwira ntchito ku ndende za m’chigawochi kuti adzipereka thumba la chimanga la 50...