Unduna wa za maboma ang’ono, umodzi ndi chikhalidwe wapempha akubanja kwa malemu mfumu Mgulumia ku Machinga kuti atsate ndondomeko zonse zoyenera posankha mfumu ina yatsopano....
M’busa Thomson John Chipeta, yemwe anakhazikitsa Home of Hope Orphanage, m’boma la Mchinji wati mabvuto akulu omwe akukumananawo ndi kuchepa kwa chakudya komanso zipangizo zophunzitsira...
Nduna yoona za chisamaliro cha anthu, a Jean Sendeza, lero ikuyendera Hope Orphanage, m’boma la Mchinji kuti imve ena mwa mavuto amene ana komanso akuluakulu...
Bungwe la Malawi Bureau of Standards (MBS) latsegulanso sitolo ya Ekhaya ya ku Kanengo mu mzinda wa Lilongwe. Lolemba, bungweli linatseka sitoloyi ndi zina zinayi...
Ofalitsa nkhani ku bungwe la Malawi Bureau of Standards (MBS), a Wazamazama Katatu, ati bungweli likutsegula sitolo zimene eni ake awaitana kuti akonza mavuto amene...
M’modzi mwa amayi ochita bizinesi zing’onozing’ono m’dziko muno, a Fatuma Mateyu, alandira mphotho ya galimoto ya Mitsubishi Xpander ya mtengo osachepera K60 million pamapeto a...
Akuluakulu oyendetsa zamasewero mchigawo chakumpoto ati akhwimitsa malamulo kuti matimu amene akusewera mu chikho cha Mzuzu FAM under 21 League akhale okhawo amene ndi achisodzera...
Oyendetsa ndi kukonza Ku Mingoli Bash, a Sound Addicts Live, ati mwambowu udzachitika m’chaka cha 2026 m’malo mwa chaka chino ku Cape Maclear m’boma la...
Apolisi munzinda wa Lilongwe amanga a Justin Mataka, 27, powaganizira kuti anaba makina opimira amayi oyembekezera pa chipatala cha Bwaila. A Mataka, amene anayamba kugwira...
Mmodzi mwa anthu amene akufuna udindo wa wapampando ku bungwe la Northern Region Football Association (NRFA), a Masiya Nyasulu, ati ayika mfundo zokhwima zofuna kusintha...