Malawi Broadcasting Corporation
Nkhani

A Chakwera ali mu mzinda wa Mzuzu

Prezidenti Dr Lazarus Chakwera wauza anthu amchigawo chakumpoto kuti boma lake ladzipereka potukula miyoyo ya anthu mdziko muno kudzanso mchigawochi.

Dr Chakwera amalankhula pa Katoto mu mzinda wa Mzuzu pofika mchigawochi komwe khwimbi linasonkhana pomulandira.

Mtsogoleriyu wapemphanso anthu mdziko muno kuti alimbikitse umodzi.

Print Friendly, PDF & Email

Related posts

Tilime mbewu zambiri zopilira ku n’gamba — Bushiri

MBC Online

Chitukuko chisaononge chilengedwe

Davie Umar

Flames yakale isewera ndi Zambia yakale

MBC Online
error: All Content is protected. Copyright © 2022. Malawi Broadcasting Corporation. All Right Reserved.