Nduna yoona kuti pasamakhale kusiyana pantchito pakati pa amuna ndi akazi, a Jean Sendeza, ati kukhazikitsidwa kwa mtukula pakhomo wa m’mizinda ndi chitsimikizo choti mtsogoleri...
Boma likukhazikitsa mtukula pakhomo wammizinda lero. Ntchito yokhazikitsa ntchito ya mtukula pakhomo wa mmizinda,imene ndiya ndalama zokwana K15.7 billion, ili mkati mu mzinda wa Zomba....
Mlangizi wa zamaphunziro ku Zone ya Kabuthu ku Lilongwe, a Efrida Ndau, walimbikitsa aphunzitsi a msukulu za primary m’dziko muno kuphunzitsa ophunzira awo m’magulu. Malinga...
Pomwe anthu akupitilira kuvutika ndi njala kuchigwa cha mtsinje wa Shire, Mneneri Shepherd Bushiri wapereka chimanga mdera la mfumu yaikulu Mbenje m’boma la Nsanje. Thandizo...
Nduna yoona zamadzi ndi ukhondo, a Abida Mia, yadzudzula mchitidwe owononga ma pipe a amadzi komanso kuba zipangizo zothandizira kugawa madzi m’dziko muno. A Mia...
Boma mawa likhazikitsa mtukula pakhomo wa m’mizinda wa ndalama zokwana K15.7 billion. Malinga ndi m’modzi mwa akuluakulu ku unduna wa zachuma, a Kate Langwe, mwambo...
A Polisi m’boma la Chiradzulu anjata a John Mapoko a zaka 30 omwe ndi m’phunzitsi pa sukulu ya pulaimale ya Mulirankhwali kaamba kowaganizira kuti anachita...
Ma Banki asanu ndi atatu a m’dziko muno apanga phindu lokwana K256.7 billion m’chaka cha 2023 chokha, boma litadulapo kale msonkho. Izi ndi malingana ndi...
Katswiri pankhani yochita zisudzo zapakanema mdziko la Nigeria, John Ikechukwu Okafor, yemwe amatchuka ndi dzina loti Mr Ibu, wamwalira munzinda wa Lagos. Malinga ndi nyumba...