Multitudes have gathered at Nthungwa Ground in the area of Traditional Authority Thula in Nkhatabay commemorating the life of former Vice President late Dr Saulos...
President wa dziko lino watsindika kufunika koti anthu m’dziko muno akhale ogwirizana komanso mwa bata ndi mtendere ndikuyika zonse mmanja mwa Chauta, pambuyo pa chiphyinjo...
Chataika Makawa wazaka 45 ali mchitokosi cha polisi ku Mangochi pomuganizira kuti wapha mkazi wake Esimy Daudi wazaka 42, amene amamukayikira kuti anali ndi chibwenzi....
Mtsogoleri wa dziko lino, Dr Lazarus Chakwera, lero akutsogolera mtundu wa aMalawi pa mapemphero apadera okondwelera kuti dziko la Malawi lakwanitsa zaka 60 pa ufulu...
Ellen Chapinduka Nyasulu, Chief Executive Officer for ICON Properties Shareholders of Malawi Stock Exchange-listed ICON Properties have expressed satisfaction with the performance of the firm...
Khonsolo ya mnzinda wa Lilongwe usiku uno ikugwira ntchito yosesa komanso kuchotsa zinyalala mu munzindawu. Mfumu yamnzindawu, a Esther Sagawa, ndiyo ikutsogolera ntchitoyi yomwe yayambira...
Seed Co has launched a first of its kind Seedney Mobile Application in Malawi, seeking to provide agricultural information and solutions to farmers at their...