Chimwendo Banda ayamika Chakwera poyika amayi m’maudindo akuluakulu
Mtsogoleri wa zokambirana mu nyumba ya malamulo, a Richard Chimwendo Banda, wayamika mtsogoleri wa dziko lino Dr Lazarus Chakwera chifukwa chokhala ndi chikhulupiliro mwa amayi

