Unduna waza malonda ndi mafakitale walamula kuti m’mwenye yemwe anatsekula shopu yake ku Area 25 mumzinda wa Lilongwe, momwe amagulitsa zinthu za hardware, akhale atatseka...
Chiwerengero cha anthu omwe amwalira atamwa mowa odziwika kuti ‘ambuye tengeni’ kwa Manase ku Blantyre tsopano chafika pa asanu ndi atatu 8. Apolisi atsimikiza kuti...
Jonathan Phillipo, mneneri wa Polisi ku Chileka Apolisi ku Chileka amanga bambo McLean Luka a zaka 24 omwe athandiza kuchiritsa okha mkazi wawo yemwe anali...
Phungu wadera la Blantyre City East, a John Bande, wapempha mafumu kuti akhale patsogolo poteteza zipangizo ndi katundu wa boma pomwe akulimbikitsa ntchito zachitukuko. A...
A polisi ati katswiri opima matupi aanthu, Charles Dzamalala, watsiriza kupima matupi a anthu omwe afa atamwa mowa wina kwa Manase ku Blantyre. Mneneri wa...
Phungu wa dera la Lilongwe Msinja South, Francis Belekanyama, watsindika zakufunika kokhazikitsa ntchito zomwe zimathandiza achinyamata kupeza zochita. Belekanyama walankhula izi pasukulu ya pulaimale ya...
Mu chinthuzi: Gift Kawalazira – Dotolo otsogolera ntchito zaumoyo ku Blantyre Akuluakulu oona za umoyo munzinda wa Blantyre ati akufufuza za achinyamata ena amene malipoti...
Ochita malonda (Mavenda) aku Nsungwi ku Area 25 mu mzinda wa Lilongwe atseka shop ya m’mwenye wina yemwe amadziwika bwino ndi dzina lakuti Farook ponena...