Bungwe la National Aids Commission (NAC) lati abambo 41 pa 100 alionse m’dziko muno samadziwa kuti ali ndi kachirombo Ka HIV komwe kamayambitsa matenda a...
Bungwe la National Water Resources Authority lati lili ndi mapulani omanga zipilala zomwe zithandize kuletsa anthu kumanga zinthu zosiyanasiyana m’phepete mwanyanja. Mkulu wabungweli, a Dwight...
Ligi ya masewero a Volleyball ya achisodzera ati ipitilira mwezi ukaoneka pa 11 April, pofuna kuti masewerowa adziyendera limodzi ndi chikhalidwe komanso zikhulupiliro. Lachitatu, bungwe...
Boma lakhazikitsa magetsi oyendera mphamvu ya dzuwa ku nyumba ya malamulo pothana ndi vuto lakuthimathima kwa magetsi lomwe limasokoneza zokambilana za aphungu. Nduna yoona zamphamvu...
Phungu wa dera la Lilongwe City South East a Ulemu Msungama wathokoza asilamu popemphelera magawo osiyanasiyana a dziko lino mu nyengo yosala kudya ndi kupemphera...
Pamene asilamu padziko lonse mawa pa 10 April 2024 akhale akuyembekezera kukondwelera Eid-Al-fitr, kusonyeza kumaliza kwa nyengo yakusala kudya ya Ramadan, gulu la achinyamata achisilamu...
Chinthuzi: tsamba la Mtukula Pakhomo Anthu okhala mu mzinda wa Blantyre, amene boma linawayika pa mndandanda wa mtukula pakhomo wammizinda, lero alandira ndalama zawo zokwana...
Akuluakulu owona zaumoyo ku Blantyre ati atulutsa kumapeto a sabata ziwiri zikubwerazi zotsatira za kafukufuku wa chenicheni chomwe chinali mu mowa omwe wapha anthu okwana...
Apolisi kuchigawo cha ku mmawa amanga Amos Kandonje wazaka 37 pomuganizira kuti ndi mmodzi mwa mbava zomwe zinathyola nyumba ya mkulu wina wamalonda m’boma la...