Bungwe la alimi a fodya la Tobacco Association of Malawi (TAMA) Trust lati alimi a fodya ndiwokondwa chaka chino kamba koti akupha makwacha ndi mitengo...
Apolisi ku Zomba amanga Frederick Masiku wazaka 46 ndi mkazi wake Fasilen Golosi wazaka 38 chifukwa chokaniza kutengera mwana wawo kuchipatala chifukwa cha chipembedzo. Mneneri...
Kampani ya Paramount Concrete Products yati sikutekeseka ndi mmene yayambira masewero season ino timu FCB Nyasa Big Bullets mu ligi ya TNM. Mkulu wa kampani...
Munthu wina, yemwe akumuganizira kuti ndi mmodzi mwa anthu omwe anaba mfuti komanso teargas pa polisi yaku Nyungwe ku Chiradzulu mwezi watha, wafa apolisi atamuombera...
Bungwe loona zachisankho la MEC lalimbikitsa mafumu amdera la mfumu yaikulu Machinjiri Ku Blantyre kuti agwire ntchito ndi mbali zonse mosakondera kuti chisankho chapadera cha...
Alimi ambiri a fodya akupitilira kusangalala ndi mitengo yabwino yomwe kampani zogula fodya zikupereka kwa alimiwa kumisika. Malinga ndi a Musaiwale Kavina, amene ndi mmodzi...
Katswiri wankhonya Limbani Masamba wabweza chipongwe chomwe adachitiridwa ndi Simeon Tcheta chaka chatha pomugonjetsa kudzera pa ma points pa nkhonya ya mtima bii yomwe inali...
Phungu wa Dera la Nsanje Lalanje, wayamikira boma pobweretsa chitukuko cha nyumba ya ma kompyuta pa sukulu ya Phokela CDSS mderalo. Phunguyi, a Gladys Ganda,...