Anthu awiri avulala ku Area 4 mu mzinda wa Lilongwe pa ngozi ya galimoto yamtundu wa truck, ZA 9051, yomwe inanyamula chimanga komanso katundu wina....
Kampani yopanga mbewu ya SeedCo yalangiza alimi kuti aguliretu mbewu zovomerezeka nyengo ya dzinja isanafike. A Dennis Mdzalimbo, omwe amaona zamalonda Ku kampaniyi anati kugula...
Ndondomeko ya chitukuko ya GESD ikumanga mlatho wa Limbe wa ndalama zokwana K200 million zomwe zithandize m’midzi ya Kadzuwa m’dera la Inkosi Bvumbwe m’boma la...
Sukulu ya ukachenjede ya Lilongwe University of Agriculture and Natural Resources yati anthu mdziko muno asiye kuika patsogolo nsima ngati chakudya chokhacho koma kuti adzitha...
Ngati njira imodzi yofuna kupititsa patsogolo ntchito za milingo mdziko muno, bungwe loona za milingo la Malawi Bureau of Standards lati linakhazikitsa ndondomeko yopereka mphatso...
Bungwe la Malawi Electoral Commission (MEC) lalangiza anthu azisudzo omwe amachita masewero pa radio za MBC mdziko muno kuti adzipereka mauthenga olimbikitsa anthu kuti adzatenge...
Wapampando wa komiti yomwe yakonza msonkhano waukulu wa chipani cha Malawi Congress a Kezzie Msukwa walangiza mamembala a chipanichi kuti apitirize kukhala pambuyo pa Prezidenti...
Boma lati anthu amene ayamba kulandira ndalama za mtukula pakhomo akhale ndi dongosolo la kagwiritsidwe ntchito ka ndalamazo pofuna kuti miyoyo yawo itukuke ntchitoyi ikamatha....