Sukulu ya luso lamanja ya Mzuzu ili pachiopsyezo chosatsegulira mwezi wa mawawu kaamba ka ngongole yoposa K65 million imene ili nayo. Mkulu wa sukuluyi, a...
Pamene dziko la Malawi likuyembekezera gawo lachiwiri la ndalama za mungongole yotchedwa Extended Credit Facility kuchokera ku bungwe la IMF, unduna wa zachuma wati ngakhale...
Wachiwiri kwa mtsogoleri wa chipani cha Malawi Congress (MCP), a Catherine Gotani Hara, wayamikira mtsogoleri wa chipanichi komanso dziko lino, Dr Lazarus Chakwera, ponena kuti...
Newly elected Youth Director for the Malawi Congress Party (MCP), Baba Steven Malondera, has urged Malawians not to forget the strides made by the Chakwera-led...
Bungwe la Malawi Blood Transfusion (MBTS) lati silikutolela magazi okwanira, ofalitsa nkhani ku bungweli m’chigawo cha pakati, a Upile Kaimvi, atero. Iwo amayankhula izi munzinda...
Bungwe la Malawi Human Rights Commission (MHRC) lapempha nthambi zosiyanasiyana kuti zithandize amayi ndi kuwalimbikitsa kuti akwanitse kutenga nawo mbali pandale. M’modzi wa akuluakulu ku...
Vuto lochedwa kubwezeretsa ndalama kwa munthu amene walakwitsa nambala pakati pa banki ndi foni, posachedwapa likhala mbiri yakale chifukwa ma banki ndi kampani za lamya...
Bungwe la Spinal Injuries Association of Malawi (SIAM) lapempha adindo a ntchito za boma kuti adzimanga ofesi zimene zikhoza kulola anthu awulumali ovutika ndi kuyenda...