Wachiwiri kwa mtsogoleri wa dziko lino Dr Michael Usi wati ndi okhumudwa ndi mchitidwe wa anthu ena amene akumaba thandizo la chimanga lomwe Boma likupereka...
Timu ya Blue Eagles yalimbikitsa mwayi wake obweleranso mu ligi yaikulu ya TNM pomwe yagonjetsa Ekas Freight Wanderers ndi zigoli zinayi kwa zero pabwalo la...
Bungwe lopereka ngongole la National Economic Empowerment Fund (NEEF) lagawa feteleza wangongole kwa alimi am’magulu komanso oima pawokha mdera la mfumu yaikulu Chimutu mboma la...
Apolisi ku Mangochi amanga amai atatu powaganizila kuti anaba zigubu za oilo wa galimoto mu sitolo ya Chipiku. Ofalitsa nkhani za polisi ya Mangochi, a...
Asodzi awiri afa panyanja ya Malawi mphenzi itawaomba, malinga ndi ofalitsa nkhani pa polisi ya Mangochi, a Amina Tepani Daudi. A Daudi ati ngoziyi yachitika...
M’modzi mwa oyimba nyimbo zauzimu m’dziko muno, Ethel Kamwendo, walangiza oyimba nyimbo zauzimu kuti asakomedwe ndi ndalama koma agwiritse maitanidwe awo pomaimba nyimbo zolimbikitsa miyoyo...
Mlembi wamkulu wa chipani cha Malawi Congress (MCP), a Richard Chimwendo Banda, wabwerezanso kunena kuti palibe amene atafe ndi njala chifukwa boma likugawa chakudya kwa...
Apolisi ya Nathenje m’boma la Lilongwe amanga a Luwashi Bakali, 26, powaganizira kuti apha mwana omupeza wazaka ziwiri. Izi zachitika m’mudzi wa Kawale kwa mfumu...