Wachiwiri kwa nduna ya za umoyo, a Noah Chimpeni, atsindika kuti dziko la Malawi liri ndikuthekera koyendetsa ntchito za umoyo popanda thandizo la dziko la...
Bungwe la Teachers Council of Malawi (TCM) lati pofika pa 1 April chaka chino lamulo ligwira ntchito kwa aphunzitsi amene sapezeka mu kaundula yemwe bungweli...
Ena mwa anthu omwe akupindula ndi ndondomeko ya Mtukula Pakhomo m’boma la Salima ayamika boma kaamba ka ndondomekoyi, yomwe akuti ikuwathandiza kusamalira makomo awo makamakanso...
Apolisi munzinda wa Lilongwe amanga a Tsisa Mbangali azaka 26, powaganizira kuti anagwililira mlamu wawo wazaka 13 ndi kumupha. Ofalitsankhani za polisi ya Lilongwe, a...
Nduna yoona za maphunziro asukulu za ukachenjede, a Jessie Kabwila, yati sukulu ya Lilongwe University of Agriculture and Natural Resources (LUANAR) ndi yofunika kwambiri pokwanilitsa...
Unduna wa zantchito, watseka mbali ina ya Makandi Tea Estate imene ili m’boma la Thyolo chifukwa chophwanya ena mwa malamulo antchito. Mbaliyi ndi kumene kuli...
Nduna yoona za maphunziro a ukachenjede, Jessie Kabwila, ati bungwe la Higher Education Students’ Loans and Grants Board (HESLGB) ndi lofunika kwambiri pokweza ntchito zamaphunziro...
Mkulu wa Malawi Broadcasting Corporation (MBC), a George Kasakula, walengeza kuti tsopano nyumba yowulutsa mawuyi makanema ake a MBC TV komanso 2 on the Go...