Ndondomeko ya mphamvu ku anthu yachiwiri akuikhazikitsa ku Lilongwe
Unduna woona maboma ang’ono ang’ono, umodzi komanso chikhalidwe mmawa uno ukukhazikitsa ndondomeko yachiwiri ya mphamvu ku anthu munzinda wa Lilongwe. Mlozo wachiwiri-wu akonzamo zovuta zina

