Area 47 Livingstonia CCAP in Lilongwe holding celebrations of the World Women’s Day of Prayer this morning. The event has attracted women from different churches
Timu ya FCB Nyasa Big Bullets lero ili ndi mdipiti (Street Parade) mumzinda wa Blantyre pomwe, mwazina, akusonyeza zikho zimene timuyi inaanyamula mu season yapitayi.
Eleven suspected members of a notorious group of youths called ‘B13’ are behind bars for allegedly disturbing classes at schools around Soche area in Blantyre.
Apolisi ku Chileka mu mzinda wa Blantyre amanga anthu anayi atapezeka ndi ndalama zachinyengo zokwana K915,000. M’neneri wa polisi ya Chileka, a Jonathan Phillipo, wati
After a protracted wrangle between Area 25 residents and the Lilongwe City Council (LCC) over land developers that had allegedly encroached a cemetery, the Council
A khonsolo yamzinda wa Lilongwe, mogwirizana ndi asilikali achitetezo, agumula ndikusalaza sitolo zimene zinaamangidwa mphepete mwa manda ku dera la Nsungwi ku Area 25 ku
Katswiri wampira wamiyendo wadziko lino Tabitha Chawinga walandira mendulo ngati osewera mogometsa m’mwezi wa February 2024 mu ligi yayikulu ya mpira wa miyendo ya amayi
President Dr Lazarus Chakwera has urged the business community to come up with innovative ways that can fuel the country’s economic growth. Addressing captains of
Realising the critical role the business community plays in the Socio-Economic development of the country, President Dr Lazarus Chakwera and First Lady Madam Monica Chakwera