Phungu wa Dera la Nsanje Lalanje, wayamikira boma pobweretsa chitukuko cha nyumba ya ma kompyuta pa sukulu ya Phokela CDSS mderalo. Phunguyi, a Gladys Ganda,
Malawi Congress Party (MCP) Director of Youth, Richard Chimwendo Banda, has emphasized that President Lazarus Chakwera is committed to ensuring that development projects reach all
Timu ya Silver Strikers idakali patsogolo pa m’ndandanda wa matimu amu TNM Super League itagonjetsa timu ya FCB Nyasa Big Bullets 1-0 Lamulungu pa bwalo
Mulhoko wamphirameto wa FCB Nyasa Big Bullets wookelhemulhiwa ni Silver Strikers vamatheelha ayo yeereyelha va Kamuzu Stadium o Blantyre. Chinsisi Maonga amulhoko wa Silver Strikers
Amaryllis Hotel General Manager Ramy Waheed has encouraged Malawian youths to unleash their innovative potential and develop ideas that align with the Malawi 2063. Waheed
Wachiwiri kwa mtsogoleri wa dziko lino Dr Saulos Chilima tsopano wafika m’dziko la Republic of Korea kumene akachite nawo msonkhano waukulu pakati pa dzikolo ndi
Masana ano matimu a FCB Nyasa Big Bullets ndi Silver Strikers akhala akuthambitsana pa bwalo la Kamuzu mu mzinda wa Blantyre. Chochititsa chidwi ndi chakuti
Kuvumba mabindula madzulo ano pa Kamuzu Institute of Sports pakati pa ziphona zazigogodo ziwiri Limbani Masamba komanso Simeon Tcheta pa nkhonya yolimbirana lamba yomwe yakonzedwa