Ndine otetezedwa tsopano, watero mnyamata waku Salima
Mnyamata wochokera dera lamfumu yaikulu Mwanza m’boma la Salima, Chinsinsi Luka, yemwe ndi alubino, tsopano wati ndiwosangalala kamba kanyumba yomwe boma lamumangira. Nyumbayi ndimbali imodzi

