A Chikosa Silungwe, omwe anali nzawo wa malemu Dr Saulos Chilima, ati malemu Dr Chilima anathandiza kumenyera kuti m’dziko muno mubwere ulamuliro wa zipani zambiri
Nduna yoona zachitetezo m’dziko la Zambia, a Ambrose Lwiji Lufuma, yati dziko lawo lili ndi chisoni chachikulu chifukwa cha imfa ya wachiwiri kwa mtsogoleli wa
Yemwe adaali m’modzi wa akuluakulu kuchipani cha Democratic Progressive m’chigawo chakumpoto ndipo adalowa chipani cha Malawi Congress (MCP), a Joe Thomas Nyirongo, wati ndikulakwa kumafalitsa
Bungwe loona za chisankho mdziko muno la MEC lati anthu amene akuyembekeza kuponya voti pa chisankho cha makhansala ku Mwasa Ward m’boma la Mangochi ndi
Nduna yazofalitsa nkhani , a Moses Kunkuyu, ati mtsogoleri wa dziko lino, Dr. Lazarus Chakwera, alamula kuti lolemba likudzali, limene lili tsiku loyika mmanda ku
Mtsogoleri wa dziko lino, Dr Lazarus Chakwera pamodzi ndi Madame Monica Chakwera, watsogolera mtundu wa aMalawi powona nkhope ya wachiwiri kwa mtsogoleri wa dziko lino,
Bambomfumu apa Parish ya St Patrick’s mu mzinda wa Lilongwe, a Henry Zulu, alangiza Akhristu m’dziko muno kuti atengere chitsanzo chabwino cha moyo wa wachiwiri
People of Nkope in Mangochi District today paid their last respects to Major Wales Aidin, an aircraft engineer who died in the Chikangawa airplane crash