Category : Nkhani
Alimi a minda yayikulu akufuna boma liwathandize
Alimi a m’mudzi wa Simone mdera la mfumu yayikulu Nankumba m’boma la Mangochi apempha boma kuti liwathandize ndi zipangizo zolimbikitsa ulimi wa mnthilira. Alimiwa, amene...
Dzatengeni ngongole za NEEF — Kabwila
Nduna yoona zamaphunziro apamwamba, a Jessie Kabwila, yati boma likulimbikitsa aliyense amene akufuna kupeza mwayi wangongole ku bungwe la National Economic Empowerment Fund (NEEF) kuti...
Ekhaya, Blue Eagles akwapulana la mulungu
Ekhaya FC yati masewero omwe ikwapulane ndi Blue Eagles mundime yotsiriza mu chikho cha K20 million King Kabvina la mulungu lino, apereka danga lounika osewera...
‘Mkumano wa Chakwera, achinyamata chikhale chiyambi’
Achinyamata m’dziko muno ati mkumano wa pakati pa mtsogoleri wa dziko lino, Dr Lazarus Chakwera ndi iwo, umene ukuyembekezeka kukhalapo mawa Lachisanu, chikhale chiyambi. Mkulu...
DoDMA ifikira aliyense
Nthambi ya Department of Disaster Management Affairs (DoDMA) yatsimikizira anthu amene njala yawakhudza m’madera ovuta kufikako m’boma la Mangochi kuti ichita chotheka kuti anthu alandire...
Chikho cha Mayor’s chafika kumapeto ku Mzuzu
Bwalo lazamasewero la Katoto lero latangwanika chifukwa kukuchitika ndime yotsiriza ya chikho cha Mayor’s cha masewero a Mpira wamiyendo komanso wamanja. Mwambowo wayamba ndi ulendo...
Tisagulise chimanga chathu chidakali kumunda —Makwangwala
Mfumu yayikulu Makwangwala ya m’boma la Ntcheu yapempha anthu kuti asagulitse mbewu zawo, kuphatikizapo chimanga, isanakwane nthawi yokolola. Mfumuyi yapempha izi potengera kuti alimi ena...
Thandizo lakulera, uchembere wabwino laphweka ku Phalombe
Atsikana komanso amayi achichepere ambiri mdera la T/A Chiwalo m’boma la Phalombe akuti tsopano akutha kupeza thandizo la kulela komanso uchembere wabwino mosavuta. Izi zikutsatira...

