Category : Nkhani
‘Tikufuna changu pantchito zachitukuko’
Wachiwiri kwa nduna yoona za ulimi, a Benedicto Chambo, wapereka mwezi umodzi ku kampani ya Sawa Group kuti ikhale itamaliza ntchito yomanga nyumba ya Water...
Chifukato cha a Chewa chithandiza mfumu Ngabu
Bungwe la Malawi Chewa Heritage lapereka zipangizo zomangira nyumba ya mfumu yayikulu Ngabu m’boma la Nsanje. Nyumba ya mfumuyi idaoonongeka ndi mphepo yamkhutho imene idawomba...
NEEF iyamba kugawa ngongole za ulimi wamthilira
Bungwe la NEEF lati liri mkati mokonza ndondomeko zoti likhale likugawa ngongole ya zaulimi wa mthirira kuyambira mwezi wa April chaka chino. Mkulu wa bungweli,...
Ulimi wamakono udzathetsa njala — Kawale
Nduna yoona za ulimi a Sam Kawale yauza alangizi kuti adzitenga gawo lalikulu losintha kaganizidwe ka anthu ndi cholinga chothana ndi vuto lakusowa kwa chakudya...
Boma lapereka makina opangira mafuta ophikira kwa alimi
Unduna wazamaboma ang’ono wapereka makina apamwamba osiyanasiyana opangira mafuta ophikira a ndalama zokwana $90,000 ku gulu la alimi la BOMFA ku Kasungu. Makinawa akuyembekezeka kupititsa...
MRCS yapereka madzi a m’mipopi ku Karonga
Bungwe la Malawi Red Cross Society (MRCS) lapereka madzi a m’mipopi kwa anthu a m’dera la mfumu yayikulu Mwirang’ombe m’boma la Karonga pofuna kulimbikitsa ukhondo....
NGORA yati K1BN ithandiza mabungwe awo kudzidalira
Mabungwe amene si aboma ayamikira boma poyika thumba lapadera la K1 bilion lothandiza ntchito za mabungwewa. Mkulu wa bungwe la Non-Governmental Organisation Regulatory Authority (NGORA),...
‘Titsitsa mitengo ya ufa wopangira bread’
Mmodzi wa akuluakulu a kampani zopanga bread za Nyanja Bakery, Olympic Bakery komanso BreadTalk, Saizi Bakali wati ndiokonzeka kutsitsa mtengo wa bread mokomera a Malawi...
Kafukufuku wati kulorena kwakula m’boma la Mangochi
Kafukufuku oona mmene anthu a m’boma la Mangochi akuchitira pa ntchito yolimbikitsa kukhala mololerana komanso mwa mtendere waonetsa kuti khalidwe lochitirana zamtopola likuchepa. Professor Kennedy...

