Bungwe la Greenbelt Authority lati ndi lokhutitsidwa ndi kuchulukwa kwa chimanga chomwe bungweli lalima ku imodzi mwa ma Mega Farm ya Chikwawa Irrigation Scheme m’boma...
Bungwe la Islamic Information Bureau munzinda wa Mzuzu lalimbikitsa achinyamata kuti akhale ndi mtima okonda kuwerenga mabuku ndi cholinga chakuti ziwathandize kuchita bwino pa maphunziro...
Achinyamata amene mmbuyomu amadalira kulandira mtukula pakhomo tsopano ndi odziyimira paokha chifukwa cha maphunziro a ntchito zamanja amene analandira kudzera ku bungwe la Comsip. Goodson...
Chipatala cha Queen Elizabeth (QECH) munzinda wa Blantyre chati tsopano makina ake atatu mwa asanu othandiza anthu amene ali ndi vuto la impsyo ayamba kugwira...
Wachiwiri kwa mtsogoleri wa dziko lino, Dr Michael Usi, walimbikitsa anthu achipembedzo cha chisilamu kuti apitirize kukhala chitsanzo chabwino pa ntchito yolimbikitsa chikondi komanso kulolerana...
Louis Masamba ndiye amusankha kukhala mtsogoleri wa National Theatre Association of Malawi (NTAM). Izi zikudza pamene anthu ochita zisudzo oposa 300 anasonkhana m’boma la Salima...
Anthu ena adzudzula maboma a m’mbuyomu kaamba kosalabadira nsewu wa Karonga-Chiweta umene boma lapereka K5 billion ku kampani ya SOS Construction kuti awukonzenso. Pothirapo ndemanga...
Bungwe la Strengthening Science and Mathematics Education in Africa (SMASE) lati dziko la Malawi lili ndi kuthekera kokhala mphika waza ulimi mu Africa pokhapokha patakhala...