Oyimba nyimbo za Afro, Emily ‘Emmie Deebo’ Zintambira wasainirana mgwirizano okhala kazembe wa kampani yopanga sopo ya Hirwa General Dealers wandalama zokwana K80 million. Emmie...
Organisers of Mpoto Awards, which recognize talent in the Northern Region, have revealed that this year’s edition will take place on November 22. One of...
Chionetsero cha kanema cha chaka chino chichitika kumapeto a mwezi wa November munzinda wa Lilongwe, m’modzi mwa akuluakulu ku bungwe la Film Association of Malawi,...
Renowned Engineer Vitumbiko Mumba is now the manager of Amidu Ellan Muonjeza, famed for the song ‘Udikerebe’. Mumba, who previously managed the late Wambali Mkandawire,...
Katswiri oyimba Dancehall, Malinga Mafia, wapepesa kwa okonda nyimbo zake kaamba kokanika kuyimba ku phwando lamayimbidwe la Illusionz lomwe likuchitikira pagombe m’boma la Mangochi. Katswiriyu...
Amene anajambula kanema wa Belinda, gulu la Remnant Lions, ati ali ndi chikhulupiliro kuti kanemayu alimbikitsa atsikana kuti asamafooke pa maphunziro ngakhale atakumana ndi mavuto,...
Director for The Remnant Lions Theatre, Tiwonge Chisiza says all is set to for the premier of the film “Belinda” at Bingu International Convention Centre...
Mwambo wa Sand Music Festival wa chaka chino siukhalapo chifukwa cha imfa ya ‘Soldier’ Lucius Banda, amene anali mkulu wa kampani imene imakonza mwambowu ya...
Inhouse Media has signed up-and-coming Afro-Pop musician, Keli P, on a three-year deal. The label’s Talent and Production Manager, Michael Mulambia, says they discovered the...
Artists Kineo & Aidfest Madness, famed for the hit ‘Yekha’ are expected to release their first Extended Playlist titled ‘Ulendo’ on Wednesday. Assistant Manager at...