Malawi Broadcasting Corporation
Entertainment Entertainment Local Local Music News

Emmie Deebo watola chikwama

Oyimba nyimbo za Afro, Emily ‘Emmie Deebo’ Zintambira wasainirana mgwirizano okhala kazembe wa kampani yopanga sopo ya Hirwa General Dealers wandalama zokwana K80 million.

Emmie Deebo anayamikira kampaniyi kaamba kamgwirizanowu ndipo wati achita zotheka kuti asaulutse koteratera.

Ofalitsa nkhani ku kampaniyi, a Klaus Chikufenji, ati mgwirizanowu ndi wamiyezi isanu ndi umodzi ndipo cholinga chake ndikufuna kutukula achinyamata pa luso lawo komanso nkhani zamalonda.

 

Related posts

SOUTH-WEST POLICE DRILL PRIMARY STUDENTS ON ROAD SAFETY

MBC Online

Eni galimoto akondwa ndi dongosolo lokonza msewu wa Makanjira

Romeo Umali

Othandiza apempha oyendetsa masewero kulondoloza bwino ndalama

Romeo Umali
error: All Content is protected. Copyright © 2022. Malawi Broadcasting Corporation. All Right Reserved.