Thupi la wachiwiri kwa mtsogoleri wadziko lino, malemu Dr Saulos Chilima, aliyika m’manda pamudzi wa Mbirimtengelenji pa Nsipe m’dera la Senior Chief Inkosi Champiti m’boma...
Oyimira akubanja kwa mayi Mary Chilima, bambo Ziliro Chiwambo, anati akuyamika mtsogoleri wa dziko lino komanso aMalawi chifukwa cha chikondi chomwe aonetsa pa zovutazi. Iwo...
Galimoto yomwe yanyamula malemu Dr Saulos Chilima kubwalo lazamasewero la Bingu National lanyamuka pa mdipiti kupita kumudzi kwawo kwa Mbirimtengerenji mdera la mfumu yaikulu Champiti...
Nduna yoona zachitetezo m’dziko la Zambia, a Ambrose Lwiji Lufuma, yati dziko lawo lili ndi chisoni chachikulu chifukwa cha imfa ya wachiwiri kwa mtsogoleli wa...
Yemwe adaali m’modzi wa akuluakulu kuchipani cha Democratic Progressive m’chigawo chakumpoto ndipo adalowa chipani cha Malawi Congress (MCP), a Joe Thomas Nyirongo, wati ndikulakwa kumafalitsa...
Mkulu waza chipembedzo kulikulu la apolisi mdziko muno ku Area 30, Bambo mfumu Steven Likhutcha wapempha a Malawi onse kuti agwilane manja panthawi yomwe dziko...