Thupi la malemu Patricia Shanil Dzimbiri alitengera ku mudzi kwa Mfulanjobvu, kwa Kangamkundi m’dera la mfumu yayikulu Chamthunya m’boma la Balaka komwe akaliyike m’manda. Kuyambira...
Anthu ochuluka asonkhana ku nyumba ya chisoni ya Sunset Funeral Services ku Kanengo munzinda wa Lilongwe komwe pali chikonzero chonyamula ena mwa matupi a anthu...
Mkulu wa kampani ya Airtel Malawi, Charles Kamoto, wati malemu Dr Saulos Chilima anali munthu wodzipereka ndi wokonda ntchito. Poyankhula ndi MBC, a Kamoto ati...
FIFA President Gianni Infantino has offered his condolences to madam Mary Chilima, wife to the Vice President, late Dr Saulos Chilima, at their Area 12...
Bambo mfumu Henry Zulu aku St. Patrick Parish ku Area 18 ati malemu Dr Saulos Chilima anali olimbikira pogwira ntchito zampingo komanso kutumikira dziko. Iwowa...
Mtsogoleri wa zipani zotsutsa kunyumba ya malamulo, a George Chaponda, wati ali ndi chisoni chifukwa cha imfa ya wachiwiri kwa mtsogoleri wa dziko lino, Malemu...
Anthu osiyanasiyana ayamba kufika kunyumba ya wachiwiri kwa mtsogoleri wadziko lino, Malemu Dr Saulos Chilima, ku Area 12 munzinda wa Lilongwe. Ena mwa anthuwa ndi...
UTM Secretary General Patricia Kaliati has called for intensified search for the missing aircraft MAF T03 carrying Vice President Dr Saulos Chilima and nine others....