A polisi ati katswiri opima matupi aanthu, Charles Dzamalala, watsiriza kupima matupi a anthu omwe afa atamwa mowa wina kwa Manase ku Blantyre. Mneneri wa...
The World Economics Business Insider Africa has ranked Malawi among the ten best governed nations in Africa. Mauritius tops the list as the best governed...
Boma likukhazikitsa mtukula pakhomo wammizinda lero. Ntchito yokhazikitsa ntchito ya mtukula pakhomo wa mmizinda,imene ndiya ndalama zokwana K15.7 billion, ili mkati mu mzinda wa Zomba....
M’buyomu: Ma Bishop a mpingo wakatolika ndi mtsogoleri wa dziko lino, Dr Lazarus Chakwera. Boma lati lipitiriza kuyankhulana komanso kumvana ndi ma Bishop a mpingo...
File photo: Catholic Bishops posing with President Lazarus Chakwera [Credit: State House] The Government says it will continue engaging Catholic Bishops to achieve the social...
Mmodzi mwa anthu amene amayankhulapo pa nkhani zosiyanasiyana, maka zolimbikitsa ulamuliro wabwino, a Undule Mwakasungula, ati dongosolo la zachuma lomwe alipereka mnyumba ya malamulo lachisanu...
A social and governance commentator Undule Mwakasungula has described the 2024/25 national budget statement as a game changer in sustaining the gains made in Malawi’s...
A polisi amanga munthu mmodzi ogwira ntchito ku bungwe la ADMARC ndi ena awiri powaganizila kuti anazembetsa matumba a chimanga okwana 300 m’boma la Machinga....