Deputy Inspector General of Police responsible for Administration, Happy Mkandawire, says the Malawi Police Service is appreciative of the government’s commitment to improving the country’s...
Wachiwiri kwa mtsogoleri wa dziko lino Dr Michael Usi ati ndi okhumudwa kuti ena mwa aphungu anyumba ya malamulo sakuonetsa chidwi chogwiritsa ntchito ndalama zonse...
Green Climate Fund (GCF) has approved $52.3 million dollars ( approximately K91 billion) to support Malawi’s adaptation and resilient project. Food and Agriculture Organisation (FAO)...
Ntchito yosindikiza ma Passport tsopano iyambanso mawa lachitatu ku Blantyre, Nthambi yoona zolowa ndikutuluka m’dziko muno, ya Immigration, yatsimikiza zimenezi. Mneneri wa nthambiyi, a Wellington...
Thupi la yemwe anali muulutsi ku MBC, mayi Everess Kayanula, anyamuka nalo mawa kuchoka ku Blantyre kupita kumudzi kwawo kwa Msiro, mfumu yayikulu Kayembe m’boma...
President Dr Lazarus Chakwera has paid tribute to legendary artist ‘soldier’ Lucius Banda, who before his demise on Sunday served as the Presidential Advisor on...
Bungwe la Chiwalo Youth Network lalangiza achinyamata a m’boma la Phalombe kuti athandize kulimbikitsa ukhondo m’makomo mwawo komanso m’malo a boma monga ku Polisi ndi...