Mtsogoleri wa dziko lino, Dr. Lazarus Chakwera, masana ano akuyembekezeka kucheza ndi ochita malonda ochokera mmisika yosiyanasiyana ya kuchigawo chakummawa kwa dziko lino. Ochita malonda
Msonkhano wa bishop a maiko a Malawi, Zambia komanso Zimbabwe watha m’boma la Salima pomwe agwirizana zogwilira limodzi komanso kutumikira mokomera nkhosa zao maikowo pa
Malawi Defence Force Commander General Paul Verentino Phiri has stressed the importance of collaborative efforts to address issues of human trafficking and illegal migration in
Anthu oposa 146,000 a m’maboma a Ntcheu ndi Balaka akuyembekezeka kukhala ndi madzi abwino komanso aukhondo kudzera ku ntchito yopopa madzi mu nthaka pogwiritsa ntchito
Mwini wake wa kampani imene imagulitsa zipangizo zophodera za amayi ya the Nail Room, Atupele Chindevu, wati adzithandiza ligi ya chigawo chapakati yampira wamanja popereka
Olemba: Timothy Kateta Zokonzekera za mwambo wa misa yapadera yokumbukira yemwe adali wachiwiri kwa mtsogoleri wadziko lino, malemu Dr Saulos Chilima, zili mkati ku Nsipe
Minister of Trade Sosten Gwngwe has described the inauguration of the Mwanza One Stop Border Post as a game changer to the socio-economic development of