Apolisi ku Mangochi amanga oyimba odziwika kuti Bandera koma dzina lake lenileni ndi Abdul-Karim Saidi pomuganizira kuti anasunga mokakamiza mtsikana wachichepere wazaka 14. Ofalitsankhani za
National Police publicist, Peter Kalaya, has confirmed the arrest of Democratic Progressive Party (DPP) MP and former finance minister Joseph Mwanamvekha as well as four
Authorities from Chitipa and Karonga district councils as well as Civil Society leaders have signed a Community Development Agreement with Lotus Africa Limited over Kayelekera
Mtsogoleri wakale wa bungwe la Film Association of Malawi (FAMA), a Gift Sukali, wafunira zabwino atsogoleri atsopano amene bungweli lawasankha kumene. A Sukali ati ndi
Government has launched Chikoma Junior Primary School in Dedza District in a bid to reduce the distance learners walk to access basic primary education. Traditional
Bungwe la Malawi Network of Older Persons’ Organizations (MANEPO) lati ndi lokhudzidwa ndi kuchuluka kwa nkhanza zomwe achikulire akukumana nazo m’dziko muno kuphatikizapo kuwaganizira kuti
Phungu wa kummwera kwa boma la Lilongwe, a Peter Dimba, wapempha mabungwe ndi aMalawi kuti agwirane manja ndi bungwe la National Economic Empowerment Fund (NEEF)
Phungu wa kumpoto kwa boma la Mangochi, a Benedicto Chambo, wati ma boma a m’mbuyomu anamutaya ndipo sanalabadire ukadaulo wake pa ntchito za ulimi ndi