Apolisi abalalitsa anthu omwe amachita zipolowe pa mpingo wa CCAP wa Mibawa ku Mbayani
Apolisi aponya utsi okhetsa misonzi pobalalitsa anthu omwe anayambitsa zipolowe ku tchalitchi ya mpingo wa CCAP ya M’bawa ku Mbayani mu mzinda wa Blantyre. Izi

