President Dr Lazarus Chakwera has urged the international community to assist in investigating the plane crash that claimed the lives of Vice President Dr Saulos
Nduna ya zofalitsa nkhani, a Moses Kunkuyu, yati mtsogoleri wa dziko lino Dr Lazarus Chakwera walamula nduna zake kuti zikakhale nawo ku mwambo woyika mmanda
Grief is the prevalent emotion as relatives, friends, representatives of Ntchisi District Council and communities surrounding Makwaule Village in Senior Chief Chilooko’s area await the
Matupi ena a abale asanu ndi m’modzi (6) amene adatisiya pa ngozi ya ndege ku Chikangawa m’boma la Mzimba, anyamuka kupita ku maboma osiyanasiyana kuti
Anthu ochuluka asonkhana ku nyumba ya chisoni ya Sunset Funeral Services ku Kanengo munzinda wa Lilongwe komwe pali chikonzero chonyamula ena mwa matupi a anthu
Mkulu wa kampani ya Airtel Malawi, Charles Kamoto, wati malemu Dr Saulos Chilima anali munthu wodzipereka ndi wokonda ntchito. Poyankhula ndi MBC, a Kamoto ati