Nduna ya zofalitsa nkhani, a Moses Kunkuyu, yati mtsogoleri wa dziko lino Dr Lazarus Chakwera walamula nduna zake kuti zikakhale nawo ku mwambo woyika mmanda...
Grief is the prevalent emotion as relatives, friends, representatives of Ntchisi District Council and communities surrounding Makwaule Village in Senior Chief Chilooko’s area await the...
Matupi ena a abale asanu ndi m’modzi (6) amene adatisiya pa ngozi ya ndege ku Chikangawa m’boma la Mzimba, anyamuka kupita ku maboma osiyanasiyana kuti...
Mwambo wa mapemphero uli mkati ku nyumba yachisoni ya Sunset ku Kanengo, omwe ndi mwambo wofuna kuperekeza matupi a omwe adamwalira pa ngozi ya ndege...
Anthu ochuluka asonkhana ku nyumba ya chisoni ya Sunset Funeral Services ku Kanengo munzinda wa Lilongwe komwe pali chikonzero chonyamula ena mwa matupi a anthu...
FIFA President Gianni Infantino has offered his condolences to madam Mary Chilima, wife to the Vice President, late Dr Saulos Chilima, at their Area 12...
Bambo mfumu Henry Zulu aku St. Patrick Parish ku Area 18 ati malemu Dr Saulos Chilima anali olimbikira pogwira ntchito zampingo komanso kutumikira dziko. Iwowa...
Undongosi wakisu iki Dr Lazarus Chakwera ikakisye ikomiti ya makambala iyakwendesya ulubatiko lwa mfwa ya gwakibili ku ndongosi wakisu iki Dr. Saulos Chilima. Ikambala lwakufumusya...