Kusagwira ntchito kwa malo osambitsa ziweto kwakhudza alimi m’boma la Chikhwawa
Alimi a ziweto a m’boma la Chikhwawa adandaula kaamba kakusagwira ntchito kwa malo osambitsako ziweto (dip), zomwe ati zikupereka chiopsyezo cha chigodola. Izi zadziwika pamene...

