Mfumu yaikulu Mwamulowe ya m’boma la Rumphi yapempha anthu omwe akukhala m’madera ena ochokera ku dera lake kuti adzikumbukira mavuto omwe ali kuderali ndikumachitapo kanthu....
Apolisi ku Nkhunga m’boma la Nkhotakota amanga amuna awiri powaganizira kuti amatsatsa malonda a mwana wazaka zitatu. Mneneri wapolisi ya Nkhunga, Andrew Kamanga, wati amunawo...
Nduna ya za m’dziko, a Ken Zikhale Ng’oma, yalonjeza anthu ku Nsanje kuti boma lipitilira kukhazikitsa ntchito za chitukuko m’bomali ndi cholinga chotukula bizinesi zawo....
Four teams, namely Sunbird, Beach Eagles, Vinthenga and Deep Bay have qualified for the semifinals of the HTD-FAM National Beach Soccer Championship taking place in...
Treasurer for Malawi Beach Soccer Association, Force Ngwira, has pledged K500,000 to the team that will emerge champions in the in the HTD-FAM National Beach...
Apolisi ku Limbe mu mzinda wa Blantyre ati akufufuzabe chifukwa chimene John Mwanamvekha, wazaka 26, wadziwombelera ndi mfuti. Ofalitsankhani wapolisi ku Limbe, Aubrey Singanyama, wati...
Dowa East Member of Parliament Richard Chimwendo Banda who is also Minister of Local Government Unity and Culture, has urged contractors building ICT laboratories to...