Anthu osiyanasiyana ayamba kufika kunyumba ya wachiwiri kwa mtsogoleri wadziko lino, Malemu Dr Saulos Chilima, ku Area 12 munzinda wa Lilongwe. Ena mwa anthuwa ndi
Mrongozgi wa charo chino Dr Lazarus Chakwera wati wachiwiri kwa mrongozgi wa charo chino, Dr Saulos Chilima, lumoza na wanyawo wankhondi na wanayi- 9 wafwa
Tindege tating’ono tomwe timajambula zithunzi, drone, atiulutsa m’mwamba ku Bombo kuti tithandizire pa ntchito yosaka ndege yomwe inanyamula wachiwiri kwa mtsogoleri wa dziko lino Dr
Drones have been dispatched over Bombo under Traditional Authority Kabunduli by the African Drone and Data Academy from the Malawi University of Science and Technology
Nduna ya zofalitsa nkhani a Moses Kunkuyu ati nkulakwira malamulo kumafalitsa nkhani zomwe zilibe umboni pankhani ya kusowa kwa ndege yomwe wachiwiri kwa mtsogoleri wa
UTM Secretary General Patricia Kaliati has called for intensified search for the missing aircraft MAF T03 carrying Vice President Dr Saulos Chilima and nine others.
Asilikali ankhondo adziko lino a MDF, pamodzi ndi nthambi zina za chitetezo, akufunafunabe ku Chikangawa m’boma la Mzimba ndege yomwe inanyamula wachiwiri kwa mtsogoleri wa
Wasilikali wa charo chino wa (MDF) wachali kupenja ndege iyo yikanyamula wachiwiri kwa mrongozgi wa charo chino Dr. Saulos Klaus Chilima na walala walala wanyakhe