President Dr Lazarus Chakwera is attending the second Sub-Region Conference of Catholic Bishops at Area 30 in Lilongwe. The conference which starts this morning and
Amene akonza phwando la mayimbidwe la Ku Mingoli Bash achotsa oyimba onse akunja monga Cassper Nyovest ndi Young Stunna pam’ndandanda wa oimba akuphwando la chaka
President Dr Lazarus Chakwera will attend the opening Mass for the Sub-Region Catholic Bishops Conference of Malawi, Zambia and Zimbabwe tomorrow at the Inspector General’s
Oyankhulapo pa nkhani za ndale a Undule Mwakasungula ati kuchoka kwa a Dalitso Kabambe ku chipani Democratic Progressive (DPP) kutha kukhala kukhumudwa chifukwa a Peter
Police are searching for a ‘prophet’ (name withheld) accused of orchestrating a false reincarnation of a deceased Village Headman (name withheld) from Mtandire. According to
Nduna yofalitsa nkhani a Moses Kunkuyu ati pakufunika m’gwirizano wa mphamvu pakati pa bungwe la Malawi Communications Regulatory Authority (MACRA) ndi mabungwe amene amagwira nawo
Recognising the importance of modern books in Malawi’s education system, the Civil Society Education Coalition (CESEC) has donated 1,015 books to the Malawi University of
Ophunzira ena amene akulemba mayeso a Form Four ku Mangochi achedwa kulemba mayeso awo mmawa walero kaamba kakuti mapepala a mayeso amene amafuna kulemba sanafike.