Katakwe otchaya nkhonya, Ellen Simwaka, wati wayika chidwi chofuna kutenga lamba wa World Boxing Council (WBC) akapatsidwa mpata okumana ndi amene akufunanso lambayu. Simwaka wayankhula...
Malawi National Football Team Under-20 has won their second assignment at the 2024 COSAFA Under-20 tournament after defeating Comoros 2-1 at ABB Stadium in Maputo,...
Meke Mwase amusakha ngati mphunzitsi watimu ya Mighty Mukuru Wanderers kulowa m’malo mwa Nsazurwimo Ramadan yemwe anatula pansi udindowu mwezi wa May. A Ramadan anatula...
Bungwe la Anti-Corruption Bureau (ACB) lachenjeza matimu khumi ndi awiri amene afika ndime yotsiriza yamu ligi ya Chipiku kuti asamachite katangale pamasewero awo. Chenjezoli likudza...
An Engineering company, PLMB, has contributed K3.5 million to the junior welterweight non-title bout between Hannock Phiri and Regen Champion from DRC. The fight is...
A Peter Vanasiyo, 28, achita mphumi pamene apambana K200 million pa masewero a juga otchedwa Aero amene amachititsa ndi a kampani ya BetPawa. Iwo anayikapo...
Otsatira masewero a mpira wa miyendo, Dan Chemis, akukhulupilira kuti osewera wa Silver Strikers, Charles Chipala, komanso wa Premier Bet Dedza Dynamos, Promise Kamwendo, akhala...
Assistant Tourism Officer for Likoma, Joyce Storey, says snorkeling and diving courses will help boost tourism in Lakeshore districts. During a week-long snorkeling and diving...