Ntchito yopopa madzi mu nyanja ya Malawi ichepetsa vuto la madzi ku Dowa – Chakwera
Prezidenti wa dziko lino Dr Lazarus Chakwera watsimikizira anthu m’boma la Dowa kuti ntchito yopopa madzi m’nyanja ya Malawi ithandiza kubweretsa ukhondo ndi madzi pafupi...

