Oyimba wamkazi Puleng Phoofolo pamodzi ndi munthu wina amene amayendetsa galimoto ali m’chipatala cha Boitumelo m’dziko la South Africa kutsatira ngozi imene achita dzulo masana...
Mkulu wa kampani ya Magic promotions, a Brazio Mathias, ati chilichonse chikuyenda bwino pamene akukonzekera kuti aonetse koyamba kwa aMalawi kanema wawo otchedwa “Justice” amene...
Pikho Farms in Lilongwe has unveiled Zeze and Dorothy Kingston as brand ambassadors for their community empowerment project under the Mastercard scholarship programme, which is...
Vice President Dr Michael Usi has expressed sadness over further delays in the construction works at the Blantyre Cultural Centre. Usi disclosed this after he...
Organisers of the Lake of Stars Arts Festival have named South African Amapiano sensation Sho Madjozi as one of the performers at this year’s edition...
Mobile network provider TNM has urged festival organisers in the country to embrace electronic ticket-selling systems, saying this has the potential to promote accountability. Brand...
Amene akonza phwando la mayimbidwe la Ku Mingoli Bash achotsa oyimba onse akunja monga Cassper Nyovest ndi Young Stunna pam’ndandanda wa oimba akuphwando la chaka...
Anthu amunzinda wa Blantyre anali okondwa kwambiri ataonelera maimbidwe ochititsa chidwi kuchoka kwa oimba wa chamba cha amapiano, Young Stunna, wochokera m’dziko la South Africa....
Oyimba nyimbo za uzimu ati ndi okondwa ndi momwe nzika za mu nzinda wa Lilongwe zinabwelera pa phwando la maimbidwe limene linachitikira ku Sheaffer lolemba...