MEC, oweruza a Malawi ndi Kenya aombana mitu paza milandu ya chisankho
Mkulu wamajaji m’dziko muno, a Rizine Mzikamanda, ati komiti yatsopano yoona milandu ya chisankho yomwe anayikhazikitsa idzithandiza kuyendetsa mwamsanga komanso mwachilungamo milandu yamtunduwu ikachitika. A...

