Matupi ena a abale asanu ndi m’modzi (6) amene adatisiya pa ngozi ya ndege ku Chikangawa m’boma la Mzimba, anyamuka kupita ku maboma osiyanasiyana kuti...
Mwambo wa mapemphero uli mkati ku nyumba yachisoni ya Sunset ku Kanengo, omwe ndi mwambo wofuna kuperekeza matupi a omwe adamwalira pa ngozi ya ndege...
Anthu ochuluka asonkhana ku nyumba ya chisoni ya Sunset Funeral Services ku Kanengo munzinda wa Lilongwe komwe pali chikonzero chonyamula ena mwa matupi a anthu...
FIFA President Gianni Infantino has offered his condolences to madam Mary Chilima, wife to the Vice President, late Dr Saulos Chilima, at their Area 12...
Bambo mfumu Henry Zulu aku St. Patrick Parish ku Area 18 ati malemu Dr Saulos Chilima anali olimbikira pogwira ntchito zampingo komanso kutumikira dziko. Iwowa...
Undongosi wakisu iki Dr Lazarus Chakwera ikakisye ikomiti ya makambala iyakwendesya ulubatiko lwa mfwa ya gwakibili ku ndongosi wakisu iki Dr. Saulos Chilima. Ikambala lwakufumusya...
The Malawi High Commission in Tanzania has cancelled the 2024 Malawi Investment and Trade Forum which was scheduled to commence today in Tanzania. This comes...
M’mawa uno, nduna yofalitsa nkhani, a Moses Kunkuyu, anali nawo pa mwambo operekeza maliro a Abdul Lapukeni kuchoka munzinda wa Lilongwe. A Lapukeni, omwe ndi...