Mrongozgi wa charo chino, Dr Lazarus Chakwera, wakhazikiska committee ya nduna kuti yendeske nyifwa ya wachiwiri kwa mrongozgi wa charo chino, chipondi Dr Saulos Chilima....
President Dr Lazarus Chakwera has constituted a ministerial committee to oversee the state funeral of Vice President and eight others who were killed in a...
Apolisi limodzi ndi azachipatala ayamba kunyamula matupi a anthu amene ataya miyoyo yawo pangozi ya ndege imene yagwa chapa Lunjika mu nkhalango ya Chikangawa m’boma...
Anthu osiyanasiyana ayamba kufika kunyumba ya wachiwiri kwa mtsogoleri wadziko lino, Malemu Dr Saulos Chilima, ku Area 12 munzinda wa Lilongwe. Ena mwa anthuwa ndi...
Mrongozgi wa charo chino Dr Lazarus Chakwera wati wachiwiri kwa mrongozgi wa charo chino, Dr Saulos Chilima, lumoza na wanyawo wankhondi na wanayi- 9 wafwa...
Tindege tating’ono tomwe timajambula zithunzi, drone, atiulutsa m’mwamba ku Bombo kuti tithandizire pa ntchito yosaka ndege yomwe inanyamula wachiwiri kwa mtsogoleri wa dziko lino Dr...
Drones have been dispatched over Bombo under Traditional Authority Kabunduli by the African Drone and Data Academy from the Malawi University of Science and Technology...
Nduna ya zofalitsa nkhani a Moses Kunkuyu ati nkulakwira malamulo kumafalitsa nkhani zomwe zilibe umboni pankhani ya kusowa kwa ndege yomwe wachiwiri kwa mtsogoleri wa...