A Chikosa Silungwe, omwe anali nzawo wa malemu Dr Saulos Chilima, ati malemu Dr Chilima anathandiza kumenyera kuti m’dziko muno mubwere ulamuliro wa zipani zambiri...
Nduna yoona zachitetezo m’dziko la Zambia, a Ambrose Lwiji Lufuma, yati dziko lawo lili ndi chisoni chachikulu chifukwa cha imfa ya wachiwiri kwa mtsogoleli wa...
Yemwe adaali m’modzi wa akuluakulu kuchipani cha Democratic Progressive m’chigawo chakumpoto ndipo adalowa chipani cha Malawi Congress (MCP), a Joe Thomas Nyirongo, wati ndikulakwa kumafalitsa...
Bungwe loona za chisankho mdziko muno la MEC lati anthu amene akuyembekeza kuponya voti pa chisankho cha makhansala ku Mwasa Ward m’boma la Mangochi ndi...
Mtsogoleri wa dziko lino, Dr Lazarus Chakwera pamodzi ndi Madame Monica Chakwera, watsogolera mtundu wa aMalawi powona nkhope ya wachiwiri kwa mtsogoleri wa dziko lino,...
Bambomfumu apa Parish ya St Patrick’s mu mzinda wa Lilongwe, a Henry Zulu, alangiza Akhristu m’dziko muno kuti atengere chitsanzo chabwino cha moyo wa wachiwiri...