Government has launched Chikoma Junior Primary School in Dedza District in a bid to reduce the distance learners walk to access basic primary education. Traditional
Bungwe la Malawi Network of Older Persons’ Organizations (MANEPO) lati ndi lokhudzidwa ndi kuchuluka kwa nkhanza zomwe achikulire akukumana nazo m’dziko muno kuphatikizapo kuwaganizira kuti
Phungu wa kummwera kwa boma la Lilongwe, a Peter Dimba, wapempha mabungwe ndi aMalawi kuti agwirane manja ndi bungwe la National Economic Empowerment Fund (NEEF)
Phungu wa kumpoto kwa boma la Mangochi, a Benedicto Chambo, wati ma boma a m’mbuyomu anamutaya ndipo sanalabadire ukadaulo wake pa ntchito za ulimi ndi
Gershom Nyirenda, Malawi Public Universities Students Union president Malawi Public Universities Students Union says the formation of the Ministry of Higher Education is a testament
Unduna waza umoyo wati walandira katemera wa matenda a cholera 720,185 wa mkamwa kuchokera ku bungwe laza umoyo pa dziko la World Health Organization (WHO).
Police at Jenda in Mzimba have arrested Steve Manda, 33, for impersonating a Malawi Defence Force soldier from Moyale Barracks and fraudulently stealing money from
Some Prison formations in the central region have been recognised with certificates of excellence for their exceptional performance in various aspects of prison management. Central
Mkulu wa ntchito za ndende m’chigawo cha pakati, a Bazirial Chapuwala, walamula ogwira ntchito ku ndende za m’chigawochi kuti adzipereka thumba la chimanga la 50