The Private Schools Association of Malawi (PRISAM) has launched a Savings and Credit Cooperative (SACCO) to provide financial support and empowerment to private schools and
Mmodzi wa akulu akulu mchipani cha MCP yemwenso ndi nduna yaza Chitetezo Chadziko a Ken Zikhale Ng’oma ati boma lipitiriza kutukula madera onse a dziko
Nduna ya maboma ang’ono a Richard Chimwemdo Banda yalangiza mafumu kuti adzionetsetsa kuti pali chilungamo pothandiza anthu a m’midzi. A Chimwendo Banda omwenso ndi
Membala watsopano wachipani cha Malawi Congress (MCP) a Uladi Mussa athokoza mtsogoleri wa dziko lino Dr Lazarus Chakwera chifukwa chokhulukira milandu yawo ndi ya mtsogoleli
Secretary General (SG) of the International Federation of Red Cross and Red Crescent Societies ( IFRC) Jagannath Chapagain is in the country for a four
Timu ya Silver Strikers yalemba ntchito Peter Mponda ngati mphunzitsi wa timuyi amene akulowa m’malo mwa Pieter De Jongh yemwe adatula pansi udindo wake mwezi
Bungwe la atsogoleri a mipingo la Evangelical Association of Malawi (EAM) lati a Malawi ayambe kupempherera mvula kutsatira kugwa kwa ng’amba. Mlembi wa mkulu wa
The Electricity Supply Corporation of Malawi (ESCOM) has introduced a mobile application aimed at streamlining the reporting of faults and emergencies. According to ESCOM’s Board